Vinie 265 – Tchera
Play Pause 00:00 Sorry, no results.Please try another keyword Vinie 265 – Tchera VESS 1 wane ma beib Kodi umakumbukira chiyambi chake unabwera ngati mbala mtima waine mkuuba mtima waine mkuutola Mtima waine osauswa My Lady you are so beautiful am gonna fall for you You are the one I have been looking for One […]
Vinie 265 – Tchera
VESS 1
wane ma beib
Kodi umakumbukira chiyambi chake
unabwera ngati mbala mtima waine mkuuba
mtima waine mkuutola
Mtima waine osauswa
My Lady you are so beautiful
am gonna fall for you
You are the one I have been looking for
One I have been searching for
One I have been looking, searching, looking for
BRIDGE
you dives my mind
Wabweresa chimwemwe
you are so cool and so kind
zaena usamvere
HOOk X2
khutu talitchera
takhala Pasi tavesera
Zindivuta kuzitchula
nkhawa zaine kuzitula
Not to lie you are my number 1
sekesekesekerera
Uzindikonda Dali wanga
Chonde beib osaveraa
VESS 2
ndiuze ndidziwe zizathera kuti zomwe timapanga
ndili ndimantha mchirema chosadziwa ndikachoka zomwe umapanga
ndatola my lady
ndizimukhola huny ine
uzindigwira my beib
chisakho chako Paine
ndatola my lady
Ndizimukhola huny ine
UZindigwira my beib
chisankho chako pa ine

